Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 78:69-71 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

69. Ndipo anamanga malo oyera ace ngati kaphiri,Monga dziko lapansi limene analikhazikitsa kosatha.

70. Ndipo anasankha Davide mtumiki wace,Namtenga ku makola a nkhosa:

71. Anamtenga kuja anatsata zoyamwitsa,Awete Yakobo, anthu ace, ndi Israyeli, colandira cace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 78