Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 77:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Njira yanu inali m'nyanja,Koyenda Inu nku madzi akulu,Ndipo mapazi anu sanadziwika.

20. Munatsogolera anthu anu ngati gulu la nkhosa,Ndi dzanja la Mose ndi Aroni,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 77