Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 75:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Pakuti m'dzanja la Yehova muli cikho;Ndi vinyo wace acita thobvu;Cidzala ndi zosanganizira, ndipo atsanulako:Indedi, oipa onse a pa dziko lapansi adzamwaNadzagugudiza nsenga zace.

9. Koma ine ndidzalalikira kosalekeza,Ndidzayimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo.

10. Ndipo ndidzatseteka nyanga zonse za oipa;Koma nyanga za wolungama zidzakwezeka.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 75