Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 75:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tikuyamikani Inu, Mulungu; Tiyamika, pakuti dzina lanu liri pafupi;Afotokozera zodabwiza zanu,

2. Pakuona nyengo yace ndidzaweruza molunjika.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 75