Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 73:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Indedi Mulungu acitira Israyeli zabwino,Iwo a mtima wa mbe.

2. Koma ine, ndikadagwa; Mapazi anga akadaterereka,

3. Pakuti ndinacitira nsanje odzitamandira,Pakuona mtendere wa oipa,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 73