Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 71:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Poteronso pokalamba ine ndi kukhala nazo imvi musandisiye, Mulungu;Kufikira nditalalikira mbadwo uwu za dzanja lanu,Mphamvu yanu kwa onse akudza m'mbuyo.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 71

Onani Masalmo 71:18 nkhani