Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 70:2-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Acite manyazi, nadodomeAmene afuna moyo wanga:Abwezedwe m'mbuyo, napepulidwe.Amene akonda kundicitira coipa,

3. Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi aoAmene akuti, Hede, hede.

4. Asekerere nakondwerere mwa Inu onse akufuna Inu;Nanene kosalekeza iwo akukonda cipulumutso canu,Abuke Mulungu.

5. Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi;Mundifulumirire, Mulungu:Inu ndinu mthandizi wanga ndi mpulumutsi wanga;Musacedwe, Yehova.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 70