Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 7:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Anacita dzenje, nalikumba,Nagwa m'mbuna yomwe anaikumba.

16. Cobvuta cace cidzambwerera mwini,Ndi ciwawa cace cidzamgwera pakati pamutu pace.

17. Ndidzayamika Yehova monga mwa cilungamo cace;Ndipo ndidzayimbira Yehova Wam'mwambamwamba.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 7