Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 7:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu:Mundipulumutse kwa onse akundilonda, nimundilanditse;

2. Kuti angamwetule moyo wanga ngati mkango,Ndi kuukadzula, wopanda wina wondilanditsa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 7