Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 69:34-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Zakumwamba ndi dziko lapansi zimlemekeze,Nyanja ndi zonse zoyenda m'mwemo;

35. Pakuti Mulungu adzapulumutsa Ziyoni, nadzamanga midzi ya Yuda;Ndipo iwo adzakhala komweko, likhale lao lao.

36. Ndipo mbumba ya atumiki ace idzalilandira;Ndipo iwo akukonda dzina lace adzakhalam'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 69