Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 69:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipulumutseni Mulungu;Pakuti madzi afikira moyo wanga.

2. Ndamira m'thope lozama, lopanda poponderapo;Ndalowa m'madzi ozama, ndipo cigumula candimiza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 69