Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 65:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Mubveka cakaci ndi ukoma wanu;Ndipo mabande anu akukha zakuca.

12. Akukha pa mabusa a m'cipululu;Ndipo mapiri azingika naco cimwemwe.

13. Podyetsa mpodzaza ndi zoweta;Ndipo zigwa zakutidwa ndi tirigu;Zipfuula mokondwera, inde ziyimbira.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 65