Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 65:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. M'Ziyoni akulemekezani Inu mwacete, Mulungu:Adzakucitirani Inu cowindaci.

2. Wakumva pemphero Inu,Zamoyo zonse zidzadza kwa Inu.

3. Mphulupulu zinandilaka;Koma mudzafafaniza zolakwa zathu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 65