Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 60:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Koma mwapatsa mbendera akuopa Inu,Aikweze cifukwa ca coonadi.

5. Kuti okondedwa anu alanditsidwe,Pulumutsani ndi dzanja lanu lamanja, ndipo mutibvomereze.

6. Mulungu walankhula m'ciyero cace; ndidzakondwerera:Ndidzagawa Sekemu, ndidzayesa muyeso cigwa ca Sukoti.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 60