Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 56:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Muwerenga kuthawathawa kwanga:Sungani misozi yanga m'nsupa yanu;Kodi siikhala m'buku mwanu?

9. Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine:Ici ndidziwa, kuti Mulungu abvomerezana nane.

10. Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ace:Mwa Yehova ndidzalemekeza mau ace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 56