Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 56:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mundicitire cifundo, Mulungu, pakuti anthu afuna kundimeza:Andipsinja pondithira nkhondo tsiku lonse.

2. Adani anga afuna kundimeza tsiku lonse:Pakuti ambiri andithira nkhondo modzikuza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 56