Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 55:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Cherani khutu pemphero langa, Mulungu;Ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga.

2. Mveram, ndipo mundiyankhe:Ndiliralira m'kudandaula kwanga ndi kubuula;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 55