Koma ine ndine ngati mtengo wauwisi waazitona m'nyumba ya Mulungu:Ndikhulupirira cifundo ca Mulungu ku nthawi za nthawi.