Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 47:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ombani m'manja, mitundu yonse ya anthu;Pfuulirani kwa Mulungu ndi liu la kuyimbitsa.

2. Pakuti Yehova Wam'mwambamwamba ndiye woopsa;Ndiye mfumu yaikuru pa dziko lonse lapansi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 47