Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 44:23-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Galamukani, mugoneranji, Ambuye?Ukani, musatitaye citayire.

24. Mubisiranji nkhope yanu,Ndi kuiwala kuzunzika ndi kupsinjika kwathu?

25. Pakuti moyo wathu waweramira kupfumbi:Pamimba pathu pakangamira dziko lapansi.

26. Ukani, tithandizeni,Tiomboleni mwa cifundo canu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 44