Kuti ndipite kufikira guwa la nsembe la Mulungu,Kufikira Mulungu wa cimwemwe canga ceniceni:Ndi kuti ndikuyamikeni ndi zeze, Mulungu, Mulungu wanga.