Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji?Ndimayenderanji woliralira cifukwa ca kundipsinja mdani?