Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 36:11-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Phazi la akudzikuza lisandifikire ine,Ndi dzanja la oipa lisandicotse.

12. Pomwepo padagwera ocita zopanda pace:Anawalikha, ndipo sadzatha kuukanso.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 36