Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 36:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Colakwa ca woipayo cimati m'kati mwa mtima wanga,Palibe kuopa Mulungu pamaso pace.

2. Pakud adzidyoletsa yekha m'kuona kwace,Kuti anthu sadzacipeza coipa cace ndi kukwiya naco.

3. Mau a pakamwa pace ndiwo opanda pace ndi onyenga:Waleka kuzindikira ndi kucita bwino.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 36