Mafupa anga onse adzanena, Yehova, afanana ndi Inu ndani,Wakulanditsa wozunzika kwa iye amene amposa mphamvu,Ndi wozunzika ndi waumphawi kwa iye amfunkhira?