Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 26:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda m'ungwiro wanga:Ndipo ndakhulupirira Yehova, sindidzaterereka.

2. Mundiyesere, Yehova, ndipo mundisunthe;Yeretsani imso zanga ndi mtima wanga.

3. Pakuti cifundo canu ciri pamaso panga;Ndipo ndayenda m'coona canu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 26