Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 24:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zace zomwe,Dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m'mwemo.

2. Pakuti Iye analimanga pazinyanja,Nalikhazika pamadzi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 24