Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 22:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu akuopa Yehova, mumlemekeze;Inu nonse mbumba ya Yakobo, mumcitire ulemu;Ndipo mucite mantha ndi Iye, inu nonse mbumba ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 22

Onani Masalmo 22:23 nkhani