Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 21:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Pakuti mudzawabweza m'mbuyo,Popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao,

13. Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu:Potero tidzayimba ndi kulemekeza cilimbiko canu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 21