Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 2:10-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Tsono, mafumu inu, citani mwanzeru:Langikani, oweruza inu a dziko lapansi.

11. Tumikirani Yehova ndi mantha,Ndipo kondwerani ndi cinthenthe.

12. Mpsompsoneni Mwanayo, kuti angakwiye, ndipo mungatayike m'njira,Ukayaka pang'ono pokha mkwiyo wace.Odala onse akumkhulupirira Iye.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 2