Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 19:13-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Ndiponso muletse kapolo wanu pa zodzitama;Zisacite ufumu pa ine: pamenepo ndidzakhala wangwiro,Ndi wosacimwa colakwa cacikuru.

14. Mau a m'kamwa mwanga ndi maganizo a m'mtima wanga abvomerezeke pamaso panu,Yehova, thanthwe langa, ndi Mombolo wanga,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 19