Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 19:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Zakumwamba zimalalikira ulemerero wa Mulungu;Ndipo thambo lionetsa nchito ya manja ace.

2. Usana ndi usana ucurukitsa mau,Ndipo usiku ndi usiku uonetsa nzeru.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 19