Koma ine ndidzapenyerera nkhope yanu m'cilungamo:Ndidzakhuta mtima ndi maonekedwe anu, pamene ndidzauka.