Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 150:2-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Mlemekezeni cifukwa ca nchito zace zolimba;Mlemekezeni monga mwa ukulu wace waunjinji.

3. Mlemekezeni ndi kulira kwa lipenga;Mlemekezeni ndi cisakasa ndi zeze.

4. Mlemekezeni ndi lingaka ndi kuthira mang'ombe:Mlemekezeni ndi zoyimbira za zingwe ndi citoliro.

5. Mlemekezeni ndi nsanje zomveka:Mlemekezeni ndi nsanje zoliritsa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 150