Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 150:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Haleluya,Lemekezani Mulungu m'malo ace oyera;Mlemekezeni m'thambo la mphamvu yace.

2. Mlemekezeni cifukwa ca nchito zace zolimba;Mlemekezeni monga mwa ukulu wace waunjinji.

3. Mlemekezeni ndi kulira kwa lipenga;Mlemekezeni ndi cisakasa ndi zeze.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 150