Ndipo anakweza nyanga ya anthu ace,Cilemekezo ca okondedwa ace onse;Ndiwo ana a Israyeli, anthu a pafupi pa Iye,Haleluya,