Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 147:10-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Mphamvu ya kavalo siimkonda:Sakondwera nayo miyendo ya munthu.

11. Yehova akondwera nao akumuopa Iye,Iwo akuyembekeza cifundo cace.

12. Yerusalemu, lemekezani Yehova;Ziyoni, lemekezani Mulungu wanu.

13. Popeza analimbitsa mipiringidzo ya zitseko zanu:Anadalitsa ana anu m'kati mwanu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 147