Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 146:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Haleluya;Ulemekeze Yehova, moyo wanga,

2. Ndidzalemekeza Yehovam'moyo mwanga;Ndidzayimbira zomlemekeza Mulungu wanga pokhala ndi moyo ine.

3. Musamakhulupirira zinduna,Kapena mwana wa munthu, amene mulibe cipulumutso mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 146