Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 145:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu;Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.

2. Masiku onse ndidzakuyamikani;Ndi kulemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 145