Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 141:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, ndaitana kwa Inu; ndifulumireni ine;Mundicherere khutu, pamene ndiitana kwa Inu.

2. Pempherolanga liikike ngaticofukiza pamaso panu;Kukweza manja anga kuikike ngati nsembe ya madzulo.

3. Muike mdindo pakamwa panga, Yehova;Sungani pakhomo pa milomo yanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 141