Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 137:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Mwana wamkazi wa ku Babulo, iwe amene udzapasulidwa;Wodala iye amene adzakubwezera cilangoMonga umo unaticitira ife.

9. Wodala iye amene adzagwira makanda ako,Ndi kuwaphwanya pathanthwe.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 137