Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 137:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lilime langa limamatike ku nsaya zanga,Ndikapanda kukumbukila inu;Ndikapanda kusankha YerusalemuKoposa cimwemwe canga copambana.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 137

Onani Masalmo 137:6 nkhani