Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 135:18-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Akuwapanga adzafanana nao;Inde, onse akuwakhulupirira.

19. A nyumba ya Israyeli inu, lemekezani Yehova:A nyumba ya Aroni inu, lemekezani Yehova:

20. A nyumba ya Levi inu, lemekezani Yehova:Inu akuopa Yehova, lemekezani Yehova.

21. Alemekezedwe Yehova kucokera m'Ziyoni,Amene akhala m'Yerusalemu.Haleluya,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 135