Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 134:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Taonani, lemekezani Yehova, atumiki a Yehova inu nonse,Akuimirira m'nyumba ya Yehova usiku,

2. Kwezani manja anu ku malo oyera,Nimulemekeze Yehova.

3. Yehova, ali m'Ziyoni, akudalitseni;Ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 134