Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 130:4-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Koma kwa Inu kuli cikhululukiro,Kuti akuopeni.

5. Ndilindira Yehova, moyo wanga ulindira,Ndiyembekeza mau ace.

6. Moyo wanga uyang'anira Ambuye,Koposa alonda matanda kuca;Inde koposa alonda matanda kuca.

7. Israyeli, uyembekezere Yehova;Cifukwa kwa Yehova kuli cifundo,Kwaonso kucurukira ciombolo.

8. Ndipo adzaombola IsrayeliKu mphulupulu zace zonse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 130