Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 13:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Kuti anganene mdani wanga, Ndamlaka;Ndipo angakondwere otsutsana nane posunthika ine.

5. Koma ine ndakhulupira pa cifundo canu;Mtima wanga udzakondwera naco cipulumutso canu:

6. Ndidzayimbira Yehova,Pakuti anandicitira zokoma.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 13