Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 127:4-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Ana a ubwana wace wa munthuAkunga mibvi m'dzanja lace la ciphona.

5. Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lace:Sadzacita manyazi iwo,Pakulankhula nao adani kucipata.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 127