Masalmo 124:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Akadapanda kukhala nafe Yehova,Pakutiukira anthu: Akadatimiza madziwo,Mtsinje ukadapita pa moyo wathu;