Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 124:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Akadapanda kukhala nafe Yehova,Anene tsono Israyeli;

2. Akadapanda kukhala nafe Yehova,Pakutiukira anthu:

3. Akadatimeza amoyo,Potipsera mtima wao.

4. Akadatimiza madziwo,Mtsinje ukadapita pa moyo wathu;

Werengani mutu wathunthu Masalmo 124