4. Mibvi yakuthwa ya ciphona.Ndi makara tsanya.
5. Tsoka ine, kuti ndiri mlendo m'Meseke,Kuti ndigonera m'mahema a Kedara!
6. Moyo wanga unakhalitsa nthawiPamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.
7. Ine ndikuti, Mtendere;Koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo.